歌曲

Sitigawana (feat. Faith Mussa) - Edit

試聽 聽全曲

作詞:     作曲:



A Phiri anabwela kuchoka ku Harare
A Phiri anabwela kuchoka ku Harare
Koma nkati mwa suitcase
Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase
Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza
"Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara"
A Phiri anaganiza
"Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara"

Koma nkati mwa suitcase
Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase
Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza
"Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara"
A Phiri anaganiza
"Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara"

Oh sitigawana!

Oh sitigawana!
Sitigawana
Oh sitigawana zida
Umandikondera
M'mene umandikondera
Ife sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana zida
Sitigawana
Ife sitigawana
Sitigawana
Oh sitigawana zida
Sitigawana!
Sitigawana!
Oh sitigawana zida
Umandikondera
M'mene umandikondera
Ife sitigawana zida
Sitigawana!
Sitigawana!
Oh sitigawana zida
Umandikondera
M'mene umandikondera
Anamwalira ku Dara

Koma nkati mwa suitcase
Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase
Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza
"Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara"
A Phiri anaganiza
"Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara"